ChinsApple -Freestyle

Crispy Malawi

[Intro]
Cheo Meek
Uhhhhh ooohh
Chinsapo
Mad beats
[Chorus]
Ndamva you looking for me
Mubwere ndi ma friends mundipeza Ku Chinsapo
Airforce ili clean ndavala white tee koma ndiku choka kwa Chinsapo
Ku Chinsapo
Ndili ghetto ngati Mchesi ndi Chinsapo
Nde ukazapwekesanso Chinsapo izakupanga chitsanzo

[Verse]
I pray to God my soul to keep
Kwa sumanje kwa Dzombe Kukagula weed[?]
Amandifila amandiwona pa screen
Or ndikayika drip ngat mfana wa teams[?]
Koma ndachoka kwa Chinsapo
Komwe ma babie amagomera Bado
Ngati samayaka amangofuna bundle
Gang yanga ma dentist izakuchotsa Mano

[Bridge]
Chinsapo
Chinsapo
Chinsapo
Chinsapo
Chinsapo
Chinsapo

[Chorus]
Ndamva you looking for me
Mubwere ndi ma friends mundipeza Ku Chinsapo
Airforce ili clean ndavala white tee koma ndiku choka kwa Chinsapo
Ku Chinsapo
Ndili ghetto ngati Mchesi ndi Chinsapo
Nde ukazapwekesanso Chinsapo izakupanga chitsanzo

[Verse 2]
Ndingotula ndima Gees[?]
Bola trizer I got the keys[?]
Ndipo Ukuziwa kale ndimakhala busy
Undihalla chama three mwina nditha kukhala free
Komabe Ase Ukuziwa sitinga chille
I gotta tell your straight ndisakubisile
I'm moving smart koma sindimapisila
And I'm talking shit koma sindinazipisire
Ndimamenyaso ma punch guys wina andigwire
Gist imandikhala ngati mpando
You can't walk in my shoes uzingovala sandals
Money talks mphwanga usachulutse nthano
Mukatinter ngati spe musachulutse Kano

[Chrous]
Ndamva you looking for me
Mubwere ndi ma friends mundipeza Ku Chinsapo
Airforce ili clean ndavala white tee koma ndiku choka kwa Chinsapo
Ku Chinsapo
Ndili ghetto ngati Mchesi ndi Chinsapo
Nde ukazapwekesanso Chinsapo izakupanga chitsanzo
Cheo Meek you've been killing it hihihihi

Trivia about the song ChinsApple -Freestyle by Crispy Malawi

When was the song “ChinsApple -Freestyle” released by Crispy Malawi?
The song ChinsApple -Freestyle was released in 2022, on the album “MLW Tape1”.

Most popular songs of Crispy Malawi

Other artists of