Pantalonè

Crispy Malawi, Brainlock Boi Sticx

[Intro: Crispy Malawi]
Uh-huh Uh-huh
Uh-huh uh-huh uh-huh
Tsono Nzawinner [?]
Okay

[Chorus: Crispy Malawi]
Praise the Lord
Nduwoneka bho ndavala pantaloné (Uh-huh)
Met my ex akuti "Mmh you've changed a lot"
The grind don't stop 'till you see the Benz on the parking lot

[Verse 1: Crispy Malawi]
I had no where to go, big bro didn't like my smokin' habits (habits)
Pano blessings ndi nyanja ngati ndimagona mkachasi (mkachasi)
Hit me up pa den uli ndi ufulu wofukisa tchalisi (tchalisi)
Koma fwaka ndi panja fukwa mkati muno nalesa
Utha kulinka ndi Eli Njuchi ngati ufuna malesa (malesa)
Anthu ena amatha kusintha city utawatenga ku Dedza (ku Dedza)
Koma usazafooke uzizapusha uzabooleza (uzabooleza)
Ngati siwe Jah Jah uli panja sindupembedza (sindupembedza)
Pamalo timatenthetsa (timatenthetsa), matako amagwedeza
So many fishes in the sea, Koma uziwa dollar ndi mbеta
I wanna get back to my roots kuti azandiyike mu Genеza
Ife timafilidwa ndi ana chifukwa timabhebhetsa
Sizachisinsi tiku chaser milli (mili mili)
Tikayipeza kuyipanga yambirimbiri (mbiri mbiri)
Numbers goin' crazy ndati muyimbire Phini
Tizaflipe milli tinapanga mili (mili mili)
Mhu Mhu
Tinapanga mbiri (mbiri mbiri)

[Chorus: Crispy Malawi]
Praise the Lord
Nduwoneka bho ndavala pantaloné
Met my ex akuti "Mmh you've changed a lot"
The grind don't stop 'till you see the Benz on the parking lot

[Verse 2: Lil Al]
Fresh out the chat[?] ndili-
Fresh out the chat ndili drunk and high
Highschool kid ndatopa ndikudya ma pie[?]
DM sindiyankha hie
Don't wonder why most people who do that
Amapanga waste my time
Mkazi wako amafuna azindikhalira pama thighs
Ndakakisser kati ndikumveka gin kalindi breathalyzer
Kakuti "Bwanji sumapanga condomize?"
Ndati "ndinapanga circumcise"
Ndati "ndinapanga circumcise"
Ndati "ndinapanga circumcise"
Ndati "ndinapanga circumcise"
Ndati "ndinapanga circumcise"
Ndati "ndinapanga circu" ah

Trivia about the song Pantalonè by Crispy Malawi

When was the song “Pantalonè” released by Crispy Malawi?
The song Pantalonè was released in 2024, on the album “DND”.
Who composed the song “Pantalonè” by Crispy Malawi?
The song “Pantalonè” by Crispy Malawi was composed by Crispy Malawi, Brainlock Boi Sticx.

Most popular songs of Crispy Malawi

Other artists of